Ezekieli 2:5 BL92

5 Ndipo iwowa, ngakhale akamva kapena akaleka kumva, (pakuti ndiwo nyumba yopanduka,) koma adzadziwa kuti panali mneneri pakati pao.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 2

Onani Ezekieli 2:5 nkhani