8 Koma iwe, wobadwa ndi munthu, tamvera ici ndirikunena nawe; usakhale iwewopanduka, ngati nyumba ija yopanduka; tsegula pakamwa pako, nudye comwe ndikupatsa.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 2
Onani Ezekieli 2:8 nkhani