Ezekieli 20:18 BL92

18 Ndipo ndinati kwa ana ao m'cipululu, Musamayenda m'malemba a atate anu, musawasunga maweruzo ao, kapena kudzidetsa ndi mafano ao;

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 20

Onani Ezekieli 20:18 nkhani