Ezekieli 20:20 BL92

20 muzipatulanso masabata anga, ndipo adzakhala cizindikilo pakati pa Ine ndi inu, kuti mudziwe kuti Ine ndine Yehova Mulungu wanu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 20

Onani Ezekieli 20:20 nkhani