Ezekieli 20:22 BL92

22 Koma ndinabweza dzanja langa ndi kucicita, cifukwa ca dzina langa; kuti lisaipsidwe pamaso pa amitundu, amene ndinawaturutsa pamaso pao. Ndinawakwezeranso dzanja langa m'cipululu,

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 20

Onani Ezekieli 20:22 nkhani