Ezekieli 20:32 BL92

32 ndi ici cimauka mumtima mwanu sicidzacitika, umo mukuti, Tidzakhala ngati amitundu, ngati mabanja a m'maiko, kutumikira mtengo ndi mwala.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 20

Onani Ezekieli 20:32 nkhani