Ezekieli 21:10 BL92

10 lanoledwa kuti liphetu, lituulidwa kuti linge mphezi; tisekererepo kodi? ndilo ndodo yacifumu ya mwana wanga, yopeputsa mtengo uli wonse.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 21

Onani Ezekieli 21:10 nkhani