2 Wobadwa ndi munthu iwe, lozetsa nkhope yako ku Yerusalemu, nuwabenthulire mau malo opatulikawa, nunenere dziko la Israyeli kulitsutsa;
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 21
Onani Ezekieli 21:2 nkhani