Ezekieli 21:29 BL92

29 Akuonera zopanda pace, akuombezera mabodza, lupanga likugoneka pa makosi a oipa olasidwa, amene lafika tsiku lao nthawi ya mphulupulu yotsiriza.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 21

Onani Ezekieli 21:29 nkhani