31 Ndipo ndidzakutsanulira mkwiyo wanga, ndidzakuuzira ndi moto wa kuzaza kwanga, ndidzakuperekanso m'manja mwa anthu ankharwe odziwa kuononga.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 21
Onani Ezekieli 21:31 nkhani