12 Analandira mphotho mwa iwe kukhetsa mwazi, walandira phindu loonjezerapo, wanyengerera anansi ako ndi kuwazunza, ndipo wandiiwala Ine, ati Ambuye Yehova.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 22
Onani Ezekieli 22:12 nkhani