Ezekieli 22:22 BL92

22 Monga siliva asungunuka m'kati mwa ng'anjo, momwemo inu mudzasungunuka m'kati mwace; motero mudzadziwa kuti Ine Yehova ndakutsanulirani ukali wanga.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 22

Onani Ezekieli 22:22 nkhani