Ezekieli 22:9 BL92

9 Anthu oneneza anali mwa iwe, kuti akhetse mwazi; ndipo anadya pamapiri mwa iwe, pakati pa iwe anacita zamanyazi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 22

Onani Ezekieli 22:9 nkhani