10 Iwowa anabvula umarisece wace, anatenga ana ace amuna ndi akazi, namupha iyeyu ndi lupanga; ndi dzina lace linamveka mwa akazi atamcitira maweruzo.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 23
Onani Ezekieli 23:10 nkhani