Ezekieli 23:22 BL92

22 Cifukwa cace, Oholiba, atero Ambuye Yehova, Taona ndidzakuutsira mabwenzi ako amene moyo wako wakufidwa nao, ndi kukufikitsira iwowa pozungulira ponse atsutsane nawe,

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 23

Onani Ezekieli 23:22 nkhani