29 ndipo adzacita nawe mwaudani, nadzalanda zonse udazigwirira nchito, nadzakusiya wamarisece ndi wausiwa; ndi umarisece wa zigololo zako udzabvulidwa, dama lako ndi zigololo zako zomwe.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 23
Onani Ezekieli 23:29 nkhani