33 Udzadzala ndi kuledzera ndi cisoni, ndi cikho codabwitsa ndi ca cipasuko, ndi cikho ca mkuru wako Samariya.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 23
Onani Ezekieli 23:33 nkhani