Ezekieli 23:37 BL92

37 Pakuti anacita cigololo, ndi m'manja mwao muli mwazi, ndipo anacita cigololo ndi mafano ao, nawapititsiranso pamoto ana ao amuna amene anandibalira, kuti athedwe.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 23

Onani Ezekieli 23:37 nkhani