Ezekieli 23:4 BL92

4 Ndipo maina ao ndiwo Ohola wamkuru, ndi Oholiba mng'ono wace; nakhala anga, nabala ana amuna ndi akazi. Ndipo maina ao, Samariya ndiye Ohola, ndi Yerusalemu ndiye Oholiba.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 23

Onani Ezekieli 23:4 nkhani