40 Ndiponso munatuma kuitana anthu ocokera kutali, ndiwo munawatumira mthenga; ndipo taona, anadza amenewo unasamba, cifukwa ca iwo unapaka maso ako mankhwala, ndi kubvala zokometsera;
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 23
Onani Ezekieli 23:40 nkhani