Ezekieli 23:49 BL92

49 Ndipo adzakubwezerani dama lanu, nimudzasenza macimo a mafano anu; motero mudzadziwa kuti Ine ndine Ambuye Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 23

Onani Ezekieli 23:49 nkhani