11 Pamenepo uukhazike pa makara ace opanda kanthu m'menemo, kuti utenthe, nuyake mkuwa wace; ndi kuti codetsa cace cisungunuke m'mwemo, kuti dzimbiri lace lithe.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 24
Onani Ezekieli 24:11 nkhani