Ezekieli 24:18 BL92

18 Ndipo nditalankhula ndi anthu m'mawa, madzulo ace mkazi wanga anamwalira; ndi m'mawa mwace ndinacita monga anandilamulira.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 24

Onani Ezekieli 24:18 nkhani