23 Ndi zilemba zanu zidzakhala pamitu panu, ndi nsapato zanu ku mapazi anu, simudzacita cisoni kapena kulira, koma mudzaonda ndi mphulupulu zanu, ndi kubulirana wina ndi mnzace.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 24
Onani Ezekieli 24:23 nkhani