27 Tsiku lomwelo pakamwa pako padzatsegukira wopulumukayo; mudzalankhula osakhalanso cete, momwemo udzawakhalira cizindikilo; ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 24
Onani Ezekieli 24:27 nkhani