3 Ndipo uphere nyumba yopandukayo fanizo, nunene nao, Atero Ambuye Yehova, Tereka mphika; uutereke, nuthire madzi m'menemo.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 24
Onani Ezekieli 24:3 nkhani