Ezekieli 26:12 BL92

12 Ndipo adzalanda cuma cako ndi kufunkha malonda ako, nadzagwetsa malinga ako ndi kupasula nyumba zako zofunika, nadzaponya miyala yako, ndi mitengo yako, ndi pfumbi lako, m'madzi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 26

Onani Ezekieli 26:12 nkhani