Ezekieli 26:14 BL92

14 Ndipo ndidzakuyesa pathanthwe poyera; udzakhala poyanika khoka, sadzakumanganso; pakuti Ine Yehova ndacinena, ati Ambuye Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 26

Onani Ezekieli 26:14 nkhani