Ezekieli 27:3 BL92

3 nuti kwa Turo, Iwe wakukhala polowera m'nyanja, wakucita malonda ndi mitundu ya anthu m'zisumbu zambiri, atero Ambuye Yehova, Iwe, Turo, wati, Ine ndine wokongola wangwiro.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 27

Onani Ezekieli 27:3 nkhani