30 nadzamveketsa mau ao pa iwe, nadzalira mowawa mtima, nadzathira pfumbi pamitu pao, nadzakunkhulira m'maphulusa,
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 27
Onani Ezekieli 27:30 nkhani