8 Okhala m'Zidoni ndi Arivadi ndiwo opalasa ako; anzeru ako, Turo, okhala mwa iwe, ndiwo oongolera ako.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 27
Onani Ezekieli 27:8 nkhani