9 Kodi udzanena ndithu pamaso pa iye wakupha iwe, Ine ndine Mulungu, pokhala uli munthu, wosati Mulungu, m'dzanja la iye wakupha iwe.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 28
Onani Ezekieli 28:9 nkhani