Ezekieli 29:21 BL92

21 Tsiku ilo ndidzameretsera nyumba ya Israyeli nyanga; ndipo ndidzakutsegulira pakamwa pakati pao; motero adzadziwa kuti Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 29

Onani Ezekieli 29:21 nkhani