12 Pamenepo mzimu unandinyamula, ndipo ndinamva kumbuyo kwanga mau a mkokomo waukuru, ndi kuti, Wodala ulemerero wa Yehova m'malo mwace.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 3
Onani Ezekieli 3:12 nkhani