Ezekieli 3:14 BL92

14 M'mwemo mzimu unandinyamula ndi kucoka nane; ndipo ndinamuka wowawidwa, womyuka mtima; koma dzanja la Yehova linandigwirizitsa,

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 3

Onani Ezekieli 3:14 nkhani