Ezekieli 3:24 BL92

24 Pamenepo unandilowa mzimu ndi kundiimika ndikhale ciriri; ndipo analankhula ndi ine, nanena nane, Muka, katsekedwe m'nyumba mwako.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 3

Onani Ezekieli 3:24 nkhani