Ezekieli 3:3 BL92

3 Nati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, dyetsa m'mimba mwako, nudzaze matumbo ako ndi mpukutu uwu ndakupatsawu. M'mwemo ndinaudya, ndi m'kamwa mwanga munazuna ngati uci.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 3

Onani Ezekieli 3:3 nkhani