Ezekieli 30:11 BL92

11 Iye ndi anthu ace pamodzi naye, woopsa amitundu, adzatengedwa aliononge dzikolo, nadzasololera Aigupto malupanga ao, ndi kudzaza dziko ndi ophedwa.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 30

Onani Ezekieli 30:11 nkhani