Ezekieli 30:21 BL92

21 Wabadwa ndi munthu iwe, ndatyola dzanja la Parao mfumu ya Aigupto, ndipo taona, silinamangidwa kuti lipole, kulikulunga ndi nsaru, kulilimbitsa ligwire lupanga.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 30

Onani Ezekieli 30:21 nkhani