Ezekieli 30:4 BL92

4 Ndi lupanga lidzadzera Aigupto, ndi m'Kusi mudzakhala kuwawa kwakukuru, pakugwa ophedwa m'Aigupto; ndipo adzacotsa aunyinji ace, ndi maziko ace adzagadamuka,

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 30

Onani Ezekieli 30:4 nkhani