Ezekieli 30:9 BL92

9 Tsiku ilo mithenga idzaturuka pamaso panga m'zombo kuopsa Akusi osalabadira; ndipo kudzakhala kuwawa kwakukuru pakati pao, monga tsiku la Aigupto, pakuti taona, likudza.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 30

Onani Ezekieli 30:9 nkhani