Ezekieli 31:17 BL92

17 Iwonso anatsika naye kumanda kwa iwo ophedwa ndi lupanga, ndiwo amene adakhala dzanja lace okhala mumthunzi mwace pakati pa amitundu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 31

Onani Ezekieli 31:17 nkhani