Ezekieli 31:4 BL92

4 Madzi anaumeretsa, cigumula cinaukulitsa, mitsinje yace inayenda, nizungulira munda wace, nipititsa micera yace ku mitengo yonse ya kuthengoko.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 31

Onani Ezekieli 31:4 nkhani