Ezekieli 31:8 BL92

8 Mikungudza ya m'munda wa Mulungu siinathe kuubisa, milombwasimanga nthambi zace, mifula siinanga nthawi zace; m'munda wa Mulungu munalibe mtengo wofanana nao kukoma kwace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 31

Onani Ezekieli 31:8 nkhani