Ezekieli 32:1 BL92

1 Ndipo kunali caka cakhumi ndi ciwiri, mwezi wakhumi ndi ciwiri, tsiku loyamba la mwezi, anandidzera mau a Yehova, akuti,

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 32

Onani Ezekieli 32:1 nkhani