Ezekieli 32:18 BL92

18 Wobadwa ndi munthu iwe, lirira aunyinji a Aigupto, nuwagwetsere iye ndi ana akazi a amitundu omveka kunsi kwa dziko, pamodzi ndi iwo akutsikira kudzenje.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 32

Onani Ezekieli 32:18 nkhani