Ezekieli 32:23 BL92

23 manda ao aikidwa ku malekezero a dzenje, ndi gulu lace lizinga manda ace; ophedwa onsewo adagwa ndi lupanga, amene anaopsetsa m'dziko la amoyo.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 32

Onani Ezekieli 32:23 nkhani