32 Pakuti ndinaika kuopsa kwace m'dziko la amoyo; ndipo adzaikidwa pakati pa osadulidwa, pamodzi ndi iwo ophedwa ndi lupanga, ndiye Farao ndi aunyinji ace onse, ali Ambuye Yehova.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 32
Onani Ezekieli 32:32 nkhani