Ezekieli 32:4 BL92

4 Ndipo ndidzakusiya pamtunda, ndidzakuponya kuthengo koyera, ndi kuteretsa pa iwe mbalame zonse za m'mlengalenga, ndi kukhutitsa zirombe za dziko lonse lapansi ndi iwe.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 32

Onani Ezekieli 32:4 nkhani