Ezekieli 32:9 BL92

9 Ndidzabvutanso mitima ya mitundu yambiri ya anthu, pakufikitsa Ine cionongeko cako mwa amitundu, m'maiko amene sunawadziwa.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 32

Onani Ezekieli 32:9 nkhani